Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 32:42 - Buku Lopatulika

42 Ndipo Noba ananka nalanda Kenati, ndi midzi yake, nautcha Noba, dzina lake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

42 Ndipo Noba ananka nalanda Kenati, ndi milaga yake, nautcha Noba, dzina lake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

42 Noba adapita kukalanda mzinda wa Kenati pamodzi ndi midzi yake, ndipo adautcha Noba, kutengera dzina lake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

42 Ndipo Noba analanda Kenati ndi midzi yozungulira ndi kuyitcha Noba, kutengera dzina la iye mwini.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 32:42
3 Mawu Ofanana  

Koma Abisalomu akali moyo adatenga nadziutsira choimiritsacho chili m'chigwa cha mfumu; pakuti anati, Ndilibe mwana wamwamuna adzakhala chikumbutso cha dzina langa; natcha choimiritsacho ndi dzina la iye yekha; ndipo chitchedwa chikumbutso cha Abisalomu, kufikira lero lomwe.


Mumtima mwao ayesa kuti nyumba zao zikhala chikhalire, ndi mokhala iwo ku mibadwomibadwo; atchapo dzina lao padziko pao.


Ndipo Gideoni anakwerera njira ya iwo okhala m'mahema kum'mawa kwa Noba, ndi Yogobeha, nakantha khamulo popeza khamulo linakhala lokhazikika mtima.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa