Numeri 32:41 - Buku Lopatulika41 Ndipo Yairi mwana wa Manase ananka nalanda midzi yao, naitcha Havoti-Yairi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Ndipo Yairi mwana wa Manase ananka nalanda midzi yao, naitcha Havoti-Yairi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Yairi wa fuko la Manase adapita kukalanda midzi ina naitcha Havoti-Yairi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Yairi, mwana wa Manase analanda midzi yambiri ya Giliyadi ndi kuyitcha kuti Havoti-Yairi. Onani mutuwo |