Numeri 32:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo Mose anapatsa Makiri mwana wa Manase Giliyadi; ndipo anakhala m'menemo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo Mose anapatsa Makiri mwana wa Manase Giliyadi; ndipo anakhala m'menemo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Mose adapatsa Makiri mwana wa Manase dziko la Giliyadi, ndipo Makiriyo adakhala m'dziko limenelo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Tsono Mose anapereka Giliyadi kwa Amakiri, ana a Manase, ndipo anakhala kumeneko. Onani mutuwo |