Numeri 32:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo ana a Makiri mwana wa Manase ananka ku Giliyadi, naulanda, napirikitsa Aamori anali m'mwemo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo ana a Makiri mwana wa Manase ananka ku Giliyadi, naulanda, napirikitsa Aamori anali m'mwemo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 A fuko la Makiri, mwana wa Manase, adapita kukalanda dziko la Giliyadi napirikitsa Aamori amene ankakhala m'dzikomo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Zidzukulu za Makiri mwana wa Manase zinapita ku Giliyadi kulanda mzindawo ndi kuthamangitsira kunja Aamori omwe anali kumeneko. Onani mutuwo |