Numeri 32:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo ana a Gadi ndi ana a Rubeni anayankha, nati, Monga Yehova anati kwa anyamata anu momwemo tidzachita. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo ana a Gadi ndi ana a Rubeni anayankha, nati, Monga Yehova anati kwa anyamata anu momwemo tidzachita. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Ndipo zidzukulu za Gadi ndi za Rubeni zidayankha kuti, “Ife atumiki anu tidzachita zomwe Chauta watiwuza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Agadi ndi Arubeni anayankha kuti, “Antchito anu adzachita zimene Yehova wanena. Onani mutuwo |