Numeri 32:30 - Buku Lopatulika30 koma akapanda kuoloka nanu okonzeka, akhale nao maiko aoao pakati pa inu m'dziko la Kanani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 koma akapanda kuoloka nanu okonzeka, akhale nao maiko aoao pakati pa inu m'dziko la Kanani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Koma akapanda kuwoloka nanu, atatenga zida zankhondo, adzalandira chuma chao pakati panu m'dziko la Kanani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Koma ngati sawoloka pamodzi nanu ndi zida zankhondo, ayenera kulandira cholowa chawo pamodzi ndi inu ku Kanaani. Onani mutuwo |
Koma mukayesa dziko la cholowa chanu nchodetsa, olokani kulowa m'dziko la cholowa cha Yehova m'mene chihema cha Yehova chikhalamo, nimukhale nacho cholowa pakati pa ife; koma musapikisana ndi Yehova kapena kupikisana nafe, ndi kudzimangira nokha guwa la nsembe, pamodzi ndi guwa la nsembe la Yehova Mulungu wathu.