Numeri 32:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo ana a Gadi ndi ana a Rubeni ananena ndi Mose, nati, Anyamata anu adzachita monga mbuyanga alamulira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo ana a Gadi ndi ana a Rubeni ananena ndi Mose, nati, Anyamata anu adzachita monga mbuyanga alamulira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Tsono ana a Gadi ndi ana a Rubeni adayankha Mose kuti, “Atumiki anu adzachitadi monga momwe inu mbuyathu mwalamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Agadi ndi Arubeni anati kwa Mose, “Ife antchito anu tidzachita monga mbuye wathu mwalamulira. Onani mutuwo |