Numeri 32:24 - Buku Lopatulika24 Dzimangireni mizinda ya ana anu, ndi makola a zoweta zanu; ndipo muzichite zotuluka m'kamwa mwanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Dzimangireni midzi ya ana anu, ndi makola a zoweta zanu; ndipo muzichite zotuluka m'kamwa mwanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Mangani mizinda ya ana anu, ndi makola a nkhosa zanu, koma muchitedi zimene mwalonjeza.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Amangireni akazi ndi ana anu mizinda, mangani makola a ziweto zanu, koma chitani zomwe mwalonjeza.” Onani mutuwo |