Numeri 32:26 - Buku Lopatulika26 Ana athu, akazi athu, zoweta zathu, ndi ng'ombe zathu zonse, zidzakhala komweko m'mizinda ya ku Giliyadi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ana athu, akazi athu, zoweta zathu, ndi ng'ombe zathu zonse, zidzakhala komweko m'midzi ya ku Giliyadi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Ana athu ndi akazi athu atsala ku mizinda ya Giliyadi, pamodzi ndi nkhosa zathu ndi ng'ombe zathu zomwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Ana ndi akazi athu, ziweto zathu zina ndi ngʼombe zidzatsala kuno ku mizinda ya Giliyadi, Onani mutuwo |