Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 32:20 - Buku Lopatulika

20 Ndipo Mose anati nao, Ngati mudzachita ichi, ndi kudzikonza kunkhondo pamaso pa Yehova,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Ndipo Mose anati nao, Ngati mudzachita ichi, ndi kudzikonza kunkhondo pamaso pa Yehova,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Choncho Mose adauza anthuwo kuti, “Muchite izi: mutenge zida pamaso pa Chauta ndi kupita ku nkhondo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Tsono Mose anati kwa anthuwo, “Ngati inu mudzachita zimenezi, kutenga zida zankhondo pamaso pa Yehova kuti muchite nkhondo,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 32:20
8 Mawu Ofanana  

ndi kuoloka Yordani pamaso pa Yehova okonzeka onse mwa inu, kufikira atapirikitsa adani ake pamaso pake,


Ndipo Yoswa anati kwa Arubeni, ndi Agadi, ndi hafu la fuko la Manase, ndi kuti,


Pamenepo Yoswa anaitana Arubeni ndi Agadi, ndi hafu la fuko la Manase,


Ndipo ana a Rubeni, ndi ana a Gadi, ndi hafu la fuko la Manase anabwerera, nachoka kwa ana a Israele ku Silo, ndiwo wa m'dziko la Kanani kunka ku dziko la Giliyadi, ku dziko laolao, limene anakhala eni ake, monga mwa lamulo la Yehova, mwa dzanja la Mose.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa