Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 32:21 - Buku Lopatulika

21 ndi kuoloka Yordani pamaso pa Yehova okonzeka onse mwa inu, kufikira atapirikitsa adani ake pamaso pake,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 ndi kuoloka Yordani pamaso pa Yehova okonzeka onse mwa inu, kufikira atapirikitsa adani ake pamaso pake,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Aliyense mwa inu atenge zida, ndipo aoloke mtsinje wa Yordani pamaso pa Chauta ndi kupirikitsa adani ake patsogolo pake,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 ndipo ngati nonsenu mudzapita ndi zida kuwoloka Yorodani pamaso pa Yehova mpaka atachotsa adani ake pamaso pake,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 32:21
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Mose anati nao, Ngati mudzachita ichi, ndi kudzikonza kunkhondo pamaso pa Yehova,


ndi dziko lagonjera Yehova; mutatero mudzabwerere, ndi kukhala osachimwira Yehova ndi Israele; ndipo dziko ili lidzakhala lanulanu pamaso pa Yehova.


Kumbukirani mau amene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulirani inu, kuti, Yehova Mulungu wanu akupatsani mpumulo, nadzakupatsani dziko lino.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa