Numeri 32:18 - Buku Lopatulika18 Sitidzabwerera kwathu, kufikira ana a Israele atalandira yense cholowa chake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Sitidzabwerera kwathu, kufikira ana a Israele atalandira yense cholowa chake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Sitidzabwerera kwathu mpaka Mwisraele aliyense atalandira choloŵa chake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Sitidzabwerera ku midzi yathu mpaka Mwisraeli aliyense atalandira cholowa chake. Onani mutuwo |