Numeri 32:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo anayandikiza, nati Tidzamangira zoweta zathu makola kuno, ndi ana athu mizinda; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo anayandikiza, nati Tidzamangira zoweta zathu makola kuno, ndi ana athu midzi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Tsono iwo adasendera kwa Mose namuuza kuti, “Poyamba mutilole kuti timange kuno makola a nkhosa zathu, ndi mizinda yoti ana athu azikhalamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ndipo iwo anabwera kwa Mose namuwuza kuti, “Ife tikufuna kumanga makola a ziweto zathu kuno ndi mizinda yokhalamo akazi athu ndi ana athu. Onani mutuwo |