Numeri 32:15 - Buku Lopatulika15 Pakuti mukabwerera m'mbuyo kusamtsata Iye, adzawasiyanso m'chipululu, ndipo mudzaononga anthu awa onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Pakuti mukabwerera m'mbuyo kusamtsata Iye, adzawasiyanso m'chipululu, ndipo mudzaononga anthu awa onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Pakuti ngati muleka kumtsata, Iye adzasiyanso anthu m'chipululu, ndipo inu mudzaonongetsa anthu onseŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ngati muleka kumutsata, Iye adzawasiyiranso anthu onsewa mʼchipululu ndipo mudzawonongetsa anthu onsewa.” Onani mutuwo |