Numeri 31:51 - Buku Lopatulika51 Ndipo Mose ndi Eleazara wansembe analandira golideyo kwa iwowo, ndizo zokometsera zonse zokonzeka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 Ndipo Mose ndi Eleazara wansembe analandira golideyo kwa iwowo, ndizo zokometsera zonse zokonzeka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Apo Mose ndi wansembe Eleazara adalandira golide kwa atsogoleriwo, pamodzi ndi zinthu zonse zosula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Ndipo Mose ndi wansembe Eliezara analandira kuchokera kwa atsogoleriwo golide pamodzi ndi zipangizo zonse zosula. Onani mutuwo |