Numeri 31:52 - Buku Lopatulika52 Ndipo golide yense wa nsembe yokweza ya Yehova amene anapereka kwa Yehova, wofuma kwa atsogoleri a zikwi, ndi atsogoleri a mazana, ndiwo masekeli zikwi khumi ndi zisanu ndi chimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201452 Ndipo golide yense wa nsembe yokweza ya Yehova amene anapereka kwa Yehova, wofuma kwa atsogoleri a zikwi, ndi atsogoleri a mazana, ndiwo masekeli zikwi khumi ndi zisanu ndi chimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa52 Golide yense amene iwo adapereka kwa Chauta kuchokera kwa atsogoleri a ankhondo zikwi, ndi kwa atsogoleri a ankhondo mazana, anali wolemera makilogaramu 200 yense pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero52 Golide yense wochokera kwa atsogoleri a 1,000 ndi atsogoleri a 100 zomwe Mose ndi Eliezara anapereka ngati mphatso kwa Yehova zinali zolemera makilogalamu 200. Onani mutuwo |