Numeri 31:42 - Buku Lopatulika42 Ndipo kunena za gawo la ana a Israele, limene Mose adalichotsa kwa anthu ochita nkhondowo, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Ndipo kunena za gawo la ana a Israele, limene Mose adalichotsa kwa anthu ochita nkhondowo, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Mose adagaŵa zofunkha napatsa Aisraele theka limodzi, kuchotsa pa zofunkha zonse zobwera ndi ankhondo aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Pa gawo la Aisraeli, Mose anapatula theka limodzi kuchotsa pa zolanda ku nkhondo zonse zimene zinabwera ndi ankhondo aja. Onani mutuwo |