Numeri 31:43 - Buku Lopatulika43 (ndipo gawo la khamulo ndilo nkhosa zikwi mazana atatu mphambu makumi atatu kudza zisanu ndi ziwiri mphambu mazana asanu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 (ndipo gawo la khamulo ndilo nkhosa zikwi mazana atatu mphambu makumi atatu kudza zisanu ndi ziwiri mphambu mazana asanu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Tsono gawo la Aisraele linali ili: nkhosa 337,500, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Tsono gawo la Aisraeli linali ili: nkhosa 337,500, Onani mutuwo |