Numeri 31:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo anthu anafikira zikwi khumi ndi zisanu ndi chimodzi; pamenepo msonkho wa Yehova ndiwo anthu makumi atatu mphambu awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo anthu anafikira zikwi khumi ndi zisanu ndi chimodzi; pamenepo msonkho wa Yehova ndiwo anthu makumi atatu mphambu awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Anthu analipo 16,000, ndipo 32 anali gawo la Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 anthu analipo 16,000 ndipo gawo la Yehova linali 32. Onani mutuwo |