Numeri 31:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo abulu anafikira zikwi makumi atatu ndi mazana asanu; pamenepo msonkho wa Yehova ndiwo makumi asanu ndi limodzi mphambu mmodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo abulu anafikira zikwi makumi atatu ndi mazana asanu; pamenepo msonkho wa Yehova ndiwo makumi asanu ndi limodzi mphambu mmodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Abulu analipo 30,500, ndipo 61 anali gawo la Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 abulu analipo 30,500 ndipo gawo la Yehova linali 61; Onani mutuwo |