Numeri 31:36 - Buku Lopatulika36 Ndipo limodzi la magawo awiri, ndilo gawo la iwo adatuluka kunkhondo, linafikira nkhosa zikwi mazana atatu mphambu makumi atatu kudza zisanu ndi ziwiri mphambu mazana asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndipo limodzi la magawo awiri, ndilo gawo la iwo adatuluka kunkhondo, linafikira nkhosa zikwi mazana atatu mphambu makumi atatu kudza zisanu ndi ziwiri mphambu mazana asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Gawo la ankhondo amene adapita ku nkhondo linali nkhosa 337,500, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Gawo la ankhondo amene anapita ku nkhondo linali: nkhosa 337,500, Onani mutuwo |