Numeri 31:35 - Buku Lopatulika35 ndi anthu, ndiwo akazi osadziwa mwamuna mogona naye, onse pamodzi zikwi makumi atatu ndi ziwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 ndi anthu, ndiwo akazi osadziwa mwamuna mogona naye, onse pamodzi zikwi makumi atatu ndi ziwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 ndi atsikana amene sadagonepo ndi amuna 32,000 pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 ndi atsikana omwe sanagonepo ndi mwamuna 32,000. Onani mutuwo |