Numeri 31:37 - Buku Lopatulika37 Ndi msonkho wa Yehova wankhosa ndiwo mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi awiri mphambu zisanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Ndi msonkho wa Yehova wankhosa ndiwo mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu ndi awiri mphambu zisanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 ndipo gawo la Chauta linali nkhosa 675. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 mwa zimenezi gawo la Yehova linali 675; Onani mutuwo |