Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 31:22 - Buku Lopatulika

22 Golide, ndi siliva, mkuwa, chitsulo, ndolo ndi mtovu zokha,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Golide, ndi siliva, mkuwa, chitsulo, ndolo ndi mtovu zokha,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Izi zokha, golide, siliva, mkuŵa, chitsulo, chiwaya ndi mtovu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Golide, siliva, mkuwa, chitsulo, chiwaya, mtovu

Onani mutuwo Koperani




Numeri 31:22
7 Mawu Ofanana  

Ndipo Zila, iyenso anabala Tubala-Kaini, mwini wakuphunzitsa amisiri onse a mkuwa ndi a chitsulo; mlongo wake wa Tubala-Kaini ndi Naama.


Chitsulo achitenga m'nthaka, ndi mkuwa ausungunula kumwala.


Ndipo Mose, ndi Eleazara wansembe, ndi akalonga onse a khamulo, anatuluka kukomana nao kunja kwa chigono.


Ndipo Eleazara wansembe ananena ndi ankhondo adapita kunkhondowo, Lemba la chilamulocho Yehova analamulira Mose ndi ili:


zonse zakulola moto, mupititse m'moto, ndipo zidzakhala zoyera; koma muziyeretsenso ndi madzi akusiyanitsa. Koma zonse zosalola moto, muzipititse m'madzi.


Koma siliva yense, ndi golide yense, ndi zotengera za mkuwa ndi chitsulo zikhala chopatulikira Yehova; zilowe m'mosungira chuma cha Yehova.


Koma ng'ombe ndi zofunkha za mzinda uwu Israele anadzifunkhira monga mwa mau a Yehova amene analamulira Yoswa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa