Numeri 31:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo Eleazara wansembe ananena ndi ankhondo adapita kunkhondowo, Lemba la chilamulocho Yehova analamulira Mose ndi ili: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo Eleazara wansembe ananena ndi ankhondo adapita kunkhondowo, Lemba la chilamulocho Yehova analamulira Mose ndi ili: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Tsono wansembe Eleazara adauza ankhondo amene adaapita ku nkhondowo kuti, “Lamulo limene Chauta walamula Mose ndi ili: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Tsono wansembe Eliezara anati kwa asilikali amene anapita ku nkhondo aja, “Lamulo limene Yehova anapereka kwa Mose ndi ili: Onani mutuwo |