Numeri 31:20 - Buku Lopatulika20 Muyeretse zovala zanu zonse, zipangizo zonse zachikopa, ndi zoomba zonse za ubweya wa mbuzi, ndi zipangizo zonse za mtengo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Muyeretse zovala zanu zonse, zipangizo zonse zachikopa, ndi zoomba zonse za ubweya wa mbuzi, ndi zipangizo zonse za mtengo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Muyeretse chovala chilichonse, chinthu chilichonse chachikopa, chinthu chilichonse chopangidwa ndi ubweya wambuzi, ndi chinthu chilichonse chopangidwa ndi mtengo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Muyeretsenso zovala zanu ndi china chilichonse chopangidwa ndi chikopa, ubweya wa mbuzi kapenanso ndi mtengo.” Onani mutuwo |