Numeri 31:19 - Buku Lopatulika19 Ndipo mukhale m'misasa kunja kwa chigono masiku asanu ndi awiri; aliyense adapha munthu, ndi aliyense wakukhudza wophedwa, mudziyeretse tsiku lachitatu ndi lachisanu ndi chiwiri, inu ndi andende anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndipo mukhale m'misasa kunja kwa chigono masiku asanu ndi awiri; aliyense adapha munthu, ndi aliyense wakukhudza wophedwa, mudziyeretse tsiku lachitatu ndi lachisanu ndi chiwiri, inu ndi andende anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Tsono aliyense mwa inu amene wapha munthu, kapena amene wakhudza mtembo, akhale kunja kwa mahema masiku asanu ndi aŵiri. Pa tsiku lachitatu ndi pa tsiku lachisanu ndi chiŵiri, mudziyeretse inuyo pamodzi ndi akapolo anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 “Inu nonse amene mwaphapo wina wake, kapena kukhudza aliyense amene anaphedwa mukhale kunja kwa msasa masiku asanu ndi awiri. Pa tsiku lachitatu mudziyeretse nokha pamodzi ndi akapolo anu. Onani mutuwo |