Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 31:18 - Buku Lopatulika

18 Koma ana aakazi onse osadziwa mwamuna mogona naye, asungeni ndi moyo akhale anu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Koma ana akazi onse osadziwa mwamuna mogona naye, asungeni ndi moyo akhale anu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Koma atsikana amene sadagone ndi mwamuna, muŵasunge akhale anu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 koma sungani mtsikana aliyense amene sanagonepo ndi mwamuna.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 31:18
7 Mawu Ofanana  

Ndipo mitundu ya anthu idzawatenga, ndi kuwafikitsa kumalo a kwao; ndipo a nyumba ya Israele adzakhala nao amitunduwo m'dziko la Yehova, ndi kuwayesa atumiki ndi adzakazi, ndipo amitunduwo adzatengedwa ndende, ndi amenewo anali ndende zao; ndipo Aisraele adzalamulira owavuta.


Kunena za kapolo wako wamwamuna, kapena wamkazi amene ukhala nao; azikhala a amitundu akuzungulira inu, kwa iwowa muzigula akapolo aamuna ndi aakazi.


Ndipo tsono iphani amuna onse mwa anawo, iphaninso akazi onse akudziwa mwamuna mogona naye.


Ndipo mukhale m'misasa kunja kwa chigono masiku asanu ndi awiri; aliyense adapha munthu, ndi aliyense wakukhudza wophedwa, mudziyeretse tsiku lachitatu ndi lachisanu ndi chiwiri, inu ndi andende anu.


Koma akazi ndi ana ndi ng'ombe ndi zonse zili m'mzindamo, zankhondo zake zonse, mudzifunkhire nokha; ndipo mudye zankhondo za adani anu, zimene Yehova Mulungu wanu anakupatsani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa