Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 31:17 - Buku Lopatulika

17 Ndipo tsono iphani amuna onse mwa anawo, iphaninso akazi onse akudziwa mwamuna mogona naye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndipo tsono iphani amuna onse mwa anawo, iphaninso akazi onse akudziwa mwamuna mogona naye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Nchifukwa chake tsono iphani mwana wamwamuna aliyense, ndi mkazi aliyense amene adadziŵapo ndi mwamuna.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Tsopano iphani munthu wamwamuna aliyense. Ndiponso iphani mayi aliyense amene anagonapo ndi mwamuna,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 31:17
6 Mawu Ofanana  

Koma ana aakazi onse osadziwa mwamuna mogona naye, asungeni ndi moyo akhale anu.


Ndipo pamene Yehova Mulungu wanu aupereka m'dzanja lanu, mukanthe amuna ake onse ndi lupanga lakuthwa.


nakawapereka Yehova Mulungu wanu pamaso panu, ndipo mukawakanthe; pamenepo muwaononge konse; musapangana nao pangano, kapena kuwachitira chifundo.


Ndipo msonkhano unatumizako amuna zikwi khumi ndi ziwiri, ndiwo ngwazi, nawalamulira ndi kuti, Mukani, nimuwakanthe okhala mu Yabesi-Giliyadi ndi lupanga lakuthwa, ndi akazi ndi ana aang'ono.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa