Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 31:15 - Buku Lopatulika

15 Ndipo Mose ananena nao, Kodi mwasunga ndi moyo akazi onse?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndipo Mose ananena nao, Kodi mwasunga ndi moyo akazi onse?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Mose adaŵafunsa kuti, “Chifukwa chiyani mwaŵasiya amoyo akazi onse?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Iye anafunsa kuti, “Kodi nʼchifukwa chiyani mwawaleka amoyo amayi onsewa?”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 31:15
13 Mawu Ofanana  

Atembereredwe iye amene agwira ntchito ya Yehova monyenga, atembereredwe iye amene abweza lupanga lake kumwazi.


iphanitu nkhalamba, mnyamata ndi namwali, makanda, ndi akazi; koma musayandikira munthu aliyense ali nacho chizindikiro, ndipo muyambe pamalo anga opatulika. Pamenepo anayamba ndi akuluwo anali pakhomo pa nyumba.


Ndipo Mose anakwiya nao akazembe a nkhondoyi, atsogoleri a zikwi, atsogoleri a mazana, akufuma kunkhondo adaithira.


Ndipo muja tinalanda mizinda yake yonse; ndipo tinaononga konse mizinda yonse, amuna ndi akazi ndi ana; sitinasiyapo ndi mmodzi yense.


Ndipo pamene Yehova Mulungu wanu aupereka m'dzanja lanu, mukanthe amuna ake onse ndi lupanga lakuthwa.


Koma akazi ndi ana ndi ng'ombe ndi zonse zili m'mzindamo, zankhondo zake zonse, mudzifunkhire nokha; ndipo mudye zankhondo za adani anu, zimene Yehova Mulungu wanu anakupatsani.


Motero Yoswa anakantha dziko lonse, la kumapiri, la kumwera, la kuchidikha, la kuzigwa, ndi mafumu ao onse; sanasiyepo ndi mmodzi yense; koma anaononga psiti zonse zampweya, monga Yehova Mulungu wa Israele adalamulira.


Ndi zofunkha zonse za mizinda iyi ndi ng'ombe ana a Israele anadzifunkhira; koma anakantha ndi lupanga lakuthwa anthu onse mpaka adawaononga osasiyapo ndi mmodzi yense wopuma mpweya.


Ndipo anapereka kuziononga ndi lupanga lakuthwa zonse za m'mzinda, amuna ndi akazi omwe, ana ndi nkhalamba zomwe, kudza ng'ombe, ndi nkhosa, ndi abulu, ndi lupanga lakuthwa.


Ndipo onse amene adagwa tsiku lija, amuna ndi akazi, ndiwo zikwi khumi ndi ziwiri, anthu onse a ku Ai.


Muka tsopano, nukanthe Amaleke, nuononge konsekonse zonse ali nazo, usawalekerere, koma uwaphe mwamuna ndi mkazi, mwana ndi woyamwa, ng'ombe ndi nkhosa, ngamira ndi bulu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa