Numeri 31:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Mose anakwiya nao akazembe a nkhondoyi, atsogoleri a zikwi, atsogoleri a mazana, akufuma kunkhondo adaithira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Mose anakwiya nao akazembe a nkhondoyi, atsogoleri a zikwi, atsogoleri a mazana, akufuma kunkhondo adaithira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Ndipo Mose adakwiyira akulu ankhondowo, atsogoleri olamulira ankhondo zikwi ndiponso atsogoleri olamulira ankhondo mazana, amene ankachokera ku nkhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Mose anakwiya nawo akuluakulu a magulu a ankhondowo: olamulira 1,000 ndi olamulira 100, amene ankachokera ku nkhondo. Onani mutuwo |