Numeri 31:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo Mose, ndi Eleazara wansembe, ndi akalonga onse a khamulo, anatuluka kukomana nao kunja kwa chigono. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo Mose, ndi Eleazara wansembe, ndi akalonga onse a khamulo, anatuluka kukomana nao kunja kwa chigono. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Mose ndi wansembe Eleazara, pamodzi ndi atsogoleri a mpingo, adakaŵachingamira kunja kwa zithando. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Mose, wansembe Eliezara ndi atsogoleri onse a gululo anapita kukakumana nawo kunja kwa misasa. Onani mutuwo |