Numeri 31:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo anadza nao andende, ndi zakunkhondo, ndi zofunkha, kwa Mose, ndi kwa Eleazara wansembe, ndi kwa khamu la ana a Israele, kuchigono, ku zidikha za Mowabu, zili ku Yordani pafupi pa Yeriko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo anadza nao andende, ndi zakunkhondo, ndi zofunkha, kwa Mose, ndi kwa Eleazara wansembe, ndi kwa khamu la ana a Israele, kuchigono, ku zidikha za Mowabu, zili ku Yordani pafupi pa Yeriko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsono adabwera nawo akapolowo, pamodzi ndi zonse zimene adalandazo, kwa Mose, kwa wansembe Eleazara ndi kwa mpingo wonse wa Aisraele, ku zithando za ku zigwa za Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yordani ku Yeriko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ndipo anabwera nawo akapolowo ndi zolanda ku nkhondozo kwa Mose ndi kwa wansembe Eliezara ndi kwa gulu lonse la Aisraeli ku misasa yawo ku chigwa cha Mowabu, mʼmbali mwa mtsinje wa Yorodani ku Yeriko. Onani mutuwo |