Numeri 31:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo anapita nazo zofunkha zonse, ndi zakunkhondo zonse, ndizo anthu ndi nyama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo anapita nazo zofunkha zonse, ndi zakunkhondo zonse, ndizo anthu ndi nyama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 natenga zonse zimene adalanda kunkhondoko, anthu pamodzi ndi nyama zomwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Anatenga zonse zimene analanda ku nkhondoko, anthu ndi zoweta zomwe. Onani mutuwo |