Numeri 30:11 - Buku Lopatulika11 ndipo mwamuna wake anamva, koma anakhala naye chete osamletsa, pamenepo zowinda zake zonse zidzakhazikika, ndi zodziletsa zonse anamanga nazo moyo wake zidzakhazikika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 ndipo mwamuna wake anamva, koma anakhala naye chete osamletsa, pamenepo zowinda zake zonse zidzakhazikika, ndi zodziletsa zonse anamanga nazo moyo wake zidzakhazikika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 tsono mwamuna wake nkumva, koma osamuuza kanthu mkaziyo ndiponso osamkaniza, ayenera kuchitadi zonse zimene adalumbira ndi zonse zimene adalonjeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 mwamuna wake ndi kumva kulumbira kwakeko koma osayankhulapo kanthu, osamuletsa, ayenera kuchitadi zonse zimene walumbira ndi zonse zimene walonjeza. Onani mutuwo |