Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 30:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo ngati anawinda m'nyumba ya mwamuna wake, kapena anamanga moyo wake ndi chodziletsa ndi kulumbirapo,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo ngati anawinda m'nyumba ya mwamuna wake, kapena anamanga moyo wake ndi chodziletsa ndi kulumbirapo,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 “Mkazi wokwatiwa akalonjeza nalumbira kuti adzachitadi zimene walonjeza,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 “Koma ngati mayi wokwatiwa alumbira nalonjeza kuti adzachitadi zimene walonjeza,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 30:10
4 Mawu Ofanana  

ndipo mwamuna wake anamva, koma anakhala naye chete osamletsa, pamenepo zowinda zake zonse zidzakhazikika, ndi zodziletsa zonse anamanga nazo moyo wake zidzakhazikika.


Munthu akachitira Yehova chowinda, kapena akalumbira lumbiro ndi kumangira moyo wake chodziletsa, asaipse mau ake; azichita monga mwa zonse zotuluka m'kamwa mwake.


Koma chowinda cha mkazi wamasiye, kapena mkazi wochotsedwa, zilizonse anamanga nazo moyo wake zidzamkhazikikira.


Ndipo Elikana mwamuna wake anati, Chita chimene chikukomera nukhale kufikira utamletsa kuyamwa; komatu Yehova akhazikitse mau ake. Chomwecho mkaziyo anakhala nayamwitsa mwana wake, kufikira anamletsa kuyamwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa