Numeri 30:9 - Buku Lopatulika9 Koma chowinda cha mkazi wamasiye, kapena mkazi wochotsedwa, zilizonse anamanga nazo moyo wake zidzamkhazikikira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Koma chowinda cha mkazi wamasiye, kapena mkazi wochotsedwa, zilizonse anamanga nazo moyo wake zidzamkhazikikira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 “Mkazi wamasiye kapena wosudzulidwa akalumbira kapena kulonjeza kuti adzachita kanthu kalikonse, ayenera kukachitadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Mayi wamasiye kapena wosiyidwa ukwati akalumbira kapena kulonjeza kuti adzachita kanthu kalikonse, ayenera kukachitadi. Onani mutuwo |