Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 3:48 - Buku Lopatulika

48 nupereke ndalama zimene akuposawo anaomboledwa nazo kwa Aroni ndi kwa ana ake aamuna.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

48 nupereke ndalama zimene akuposawo anaomboledwa nazo kwa Aroni ndi kwa ana ake amuna.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

48 Upatse Aroni pamodzi ndi ana ake aamuna ndalama zimenezi, kuti zikhale mtengo woombolera Aisraele a chiŵerengero chopitirira chija.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

48 Ndalama zimenezi uzipereke kwa Aaroni ndi ana ake aamuna kuti ukhale mtengo woombolera Aisraeli woonjezerawo.”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 3:48
3 Mawu Ofanana  

ulandire masekeli asanu pa munthu mmodzi; uwalandire pa muyeso wa sekeli wa malo opatulika (sekeli ndiwo magera makumi awiri);


Pamenepo Mose analandira ndalama zoombola nazo kwa iwo akuposa aja adawaombola Alevi;


Ndipo Mose anapatsa Aroni ndi ana ake ndalama zoombola nazo monga mwa mau a Yehova, monga Yehova adauza Mose.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa