Numeri 3:49 - Buku Lopatulika49 Pamenepo Mose analandira ndalama zoombola nazo kwa iwo akuposa aja adawaombola Alevi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201449 Pamenepo Mose analandira ndalama zoombola nazo kwa iwo akuposa aja adawaombola Alevi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa49 Choncho Mose adatenga ndalama zoombolera zija kwa Aisraele amene chiŵerengero chao chidapitirira chiŵerengero cha amene adaomboledwa ndi Alevi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero49 Choncho Mose anatenga ndalama zowombolera zija kuchokera kwa Aisraeli amene chiwerengero chawo chinaposa chiwerengero cha omwe anawomboledwa ndi Alevi. Onani mutuwo |