Numeri 3:47 - Buku Lopatulika47 ulandire masekeli asanu pa munthu mmodzi; uwalandire pa muyeso wa sekeli wa malo opatulika (sekeli ndiwo magera makumi awiri); Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 ulandire masekeli asanu pa munthu mmodzi; uwalandire pa muyeso wa sekeli wa malo opatulika (sekeli ndiwo magera makumi awiri); Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 utenge masekeli asiliva asanu pa munthu aliyense. Masekeliwo akhale olingana ndi masekeli asiliva a ku malo opatulika kumene sekeli imodzi ikwanira magera makumi aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 utenge masekeli asanu pa munthu aliyense. Masekeliwo akhale ofanana ndi masekeli a ku malo wopatulika, kumene sekeli imodzi imakwanira magera makumi awiri. Onani mutuwo |