Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 3:46 - Buku Lopatulika

46 Kunena za mazana awiri ndi makumi asanu ndi awiri kudza atatuwo oyamba kubadwa a ana a Israele, akuposa Alevi, akaomboledwe,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

46 Kunena za mazana awiri ndi makumi asanu ndi awiri kudza atatuwo oyamba kubadwa a ana a Israele, akuposa Alevi, akaomboledwe,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

46 Pofuna kuwombola ana achisamba 273 a Aisraele amene aposa chiŵerengero cha amuna a fuko la Levi,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

46 Pofuna kuwombola ana aamuna 273 oyamba kubadwa a Aisraeli amene anaposa chiwerengero cha aamuna a fuko la Levi,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 3:46
3 Mawu Ofanana  

Koma woyamba yense wa bulu uzimuombola ndi mwanawankhosa; ndipo ukapanda kumuombola uzimthyola khosi; koma oyamba onse a munthu mwa ana ako uziwaombola.


ndipo kunakhala, pamene Farao anadziumitsa kuti tisamuke, Yehova anawapha onse oyamba kubadwa m'dziko la Ejipito, kuyambira oyamba a anthu, kufikira oyamba a zoweta; chifukwa chake ndimphera nsembe Yehova zazimuna zoyamba kubadwa zonse; koma oyamba onse a ana anga ndiwaombola.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa