Numeri 3:43 - Buku Lopatulika43 Ndipo amuna onse oyamba kubadwa, powerenga maina, kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu, owerengedwa ao, ndiwo zikwi makumi awiri mphambu ziwiri kudza mazana awiri ndi makumi asanu ndi awiri mphambu atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Ndipo amuna onse oyamba kubadwa, powerenga maina, kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu, owerengedwa ao, ndiwo zikwi makumi awiri mphambu ziwiri kudza mazana awiri ndi makumi asanu ndi awiri mphambu atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Ndipo ana onse achisamba aamuna, potsata chiŵerengero cha maina ao, kuyambira a mwezi umodzi ndi opitirirapo, adakwanira 22,273. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Chiwerengero chonse cha ana aamuna oyamba kubadwa kuyambira a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 22, 273. Onani mutuwo |