Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -

Numeri 3:43 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

43 Chiwerengero chonse cha ana aamuna oyamba kubadwa kuyambira a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 22, 273.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

43 Ndipo amuna onse oyamba kubadwa, powerenga maina, kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu, owerengedwa ao, ndiwo zikwi makumi awiri mphambu ziwiri kudza mazana awiri ndi makumi asanu ndi awiri mphambu atatu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

43 Ndipo amuna onse oyamba kubadwa, powerenga maina, kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu, owerengedwa ao, ndiwo zikwi makumi awiri mphambu ziwiri kudza mazana awiri ndi makumi asanu ndi awiri mphambu atatu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

43 Ndipo ana onse achisamba aamuna, potsata chiŵerengero cha maina ao, kuyambira a mwezi umodzi ndi opitirirapo, adakwanira 22,273.

Onani mutuwo Koperani

Numeri 3:43
3 Mawu Ofanana  

Alevi onse amene Mose ndi Aaroni anawawerenga potsatira lamulo la Yehova monga mwa magulu a mabanja awo, amuna onse kuyambira a mwezi umodzi kapena kupitirirapo anali 22,000.

Choncho Mose anawerenga ana aamuna onse oyamba kubadwa a Aisraeli monga momwe Yehova anamulamulira.

Ndipo Yehova anawuzanso Mose kuti,

Titsatireni:

Zotsatsa

Zotsatsa