Numeri 3:42 - Buku Lopatulika42 Ndipo Mose anawawerenga, monga Yehova adamuuza, oyamba kubadwa onse mwa ana a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Ndipo Mose anawawerenga, monga Yehova adamuuza, oyamba kubadwa onse mwa ana a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Choncho Mose adaŵerenga ana onse achisamba, monga Chauta adamlamula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Choncho Mose anawerenga ana aamuna onse oyamba kubadwa a Aisraeli monga momwe Yehova anamulamulira. Onani mutuwo |