Numeri 3:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Werenga amuna oyamba kubadwa onse a ana a Israele kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu nuone chiwerengo cha maina ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Werenga amuna oyamba kubadwa onse a ana a Israele kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu nuone chiwerengo cha maina ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Chauta adauza Mose kuti, “Uŵerenge ana achisamba onse aamuna a Aisraele, kuyambira a mwezi umodzi ndi opitirirapo, potchula maina ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Yehova anawuza Mose kuti, “Werenga ana onse aamuna oyamba kubadwa mu Israeli, omwe ali ndi mwezi umodzi kapena kupitirirapo ndipo ulembe mndandanda wa mayina awo. Onani mutuwo |