Numeri 3:39 - Buku Lopatulika39 Owerengedwa onse a Alevi, adawawerenga Mose ndi Aroni, powauza Yehova, monga mwa mabanja ao, amuna mphambu, ndiwo zikwi makumi awiri mphambu ziwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Owerengedwa onse a Alevi, adawawerenga Mose ndi Aroni, powauza Yehova, monga mwa mabanja ao, amuna mphambu, ndiwo zikwi makumi awiri mphambu ziwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Alevi onse amene Mose pamodzi ndi Aroni adaŵerenga potsata mabanja ao, Chauta ataŵalamula kutero, ndiye kuti amuna onse kuyambira a mwezi umodzi ndi opitirirapo, anali 22,000. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Alevi onse amene Mose ndi Aaroni anawawerenga potsatira lamulo la Yehova monga mwa magulu a mabanja awo, amuna onse kuyambira a mwezi umodzi kapena kupitirirapo anali 22,000. Onani mutuwo |