Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 3:37 - Buku Lopatulika

37 ndi nsichi za pabwalo pozungulira, ndi makamwa ake, ndi zichiri zake, ndi zingwe zake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

37 ndi nsichi za pabwalo pozungulira, ndi makamwa ake, ndi zichiri zake, ndi zingwe zake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

37 Ankasamalanso mizati yozungulira bwalo ndi masinde ake, ndiponso zikhomo zake ndi zingwe zake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

37 pamodzi ndi mizati yozungulira bwalo ndi matsinde ake, zikhomo za chihema ndi zingwe zake.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 3:37
4 Mawu Ofanana  

Zipangizo zonse za chihema, m'machitidwe ake onse, ndi zichiri zake zonse, ndi zichiri zonse za bwalo lake, zikhale zamkuwa.


Ndipo choyang'anira iwo, udikiro wao wa ana a Merari ndiwo matabwa a chihema, ndi mitanda yake, ndi mizati ndi nsanamira zake, ndi makamwa ake, ndi zipangizo zake zonse, ndi ntchito zake zonse;


Ndipo amene adamanga mahema ao pa khomo la Kachisi, kum'mawa, pa khomo la chihema chokomanako kotulukira dzuwa, ndiwo Mose ndi Aroni, ndi ana ake aamuna, akusunga udikiro wa malo opatulika, ndiwo udikiro wa ana a Israele; koma mlendo wakuyandikizako amuphe.


Kunena za ana a Merari, Uwawerenge monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa