Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 3:33 - Buku Lopatulika

33 Banja la Amali, ndi banja la Amusi ndiwo Amerari; ndiwo mabanja a Merari.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

33 Banja la Amali, ndi banja la Amusi ndiwo a Merari; ndiwo mabanja a Merari.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

33 Amali ndi Amusi anali mabanja otuluka mwa Merari. Ameneŵa ndiwo amene anali mabanja a Merari.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

33 Kwa Merari kunali banja la Mali ndi banja la Musi. Amenewa ndiye anali mabanja a Amerari.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 3:33
7 Mawu Ofanana  

Ana a Merari: Mali ndi Musi. Ndi ana a Mali: Eleazara ndi Kisi.


Ana a Merari: Mali ndi Musi. Ndi mabanja a Alevi monga mwa nyumba za makolo ao ndi awa.


Awa ndi mabanja a Alevi: banja la Alibini, banja la Ahebroni, banja la Amali, banja la Amusi, banja la Akora. Ndipo Kohati anabala Amuramu.


Ndi ana a Merari monga mwa mabanja ao: Mali ndi Musi. Awa ndi mabanja a Alevi monga mwa nyumba za makolo ao.


Ndipo kalonga wa akalonga a Alevi ndiye Eleazara mwana wa Aroni wansembeyo; ndiye aziyang'anira osunga udikiro wa pamalo opatulika.


Ndipo owerengedwa ao, powerenga amuna onse, kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu, ndiwo zikwi zisanu ndi chimodzi kudza mazana awiri.


Kunena za ana a Merari, Uwawerenge monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa