Numeri 3:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo udikiro wao ndiwo likasa, ndi gome, ndi choikaponyali, ndi maguwa a nsembe, ndi zipangizo za malo opatulika zimene achita nazo, ndi nsalu yotchinga, ndi ntchito zake zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo udikiro wao ndiwo likasa, ndi gome, ndi choikapo nyali, ndi magome a nsembe, ndi zipangizo za malo opatulika zimene achita nazo, ndi nsalu yotchinga, ndi ntchito zake zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Ndipo ntchito imene iwo adapatsidwa inali yosamala Bokosi lachipangano, tebulo, choikaponyale, maguwa, zipangizo za m'malo opatulika zimene ansembe ankagwirira ntchito, pamodzi ndi nsalu yochingira. Ankagwira ntchito zonse zokhudza zimenezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Iwo ankagwira ntchito yosamalira Bokosi la Chipangano, tebulo, choyikapo nyale, maguwa, zipangizo za kumalo wopatulika zimene ansembe ankagwiritsa ntchito, katani, ndi zonse zomwe ankagwiritsa ntchito. Onani mutuwo |