Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 3:29 - Buku Lopatulika

29 Mabanja a ana a Kohati azimanga mahema ao pa mbali ya chihema cha kumwera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 Mabanja a ana a Kohati azimanga mahema ao pa mbali ya Kachisi ya kumwera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Mabanja a ana a Kohati ankamanga zithando zao kumwera kwa chihema cha Mulungu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Mabanja a ana a Kohati ankamanga misasa yawo kummwera kwa Chihema.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 3:29
5 Mawu Ofanana  

Koma Alevi amange mahema ao pozungulira pa chihema cha mboni, kuti mkwiyo ungagwere khamu la ana a Israele; ndipo Alevi azidikira chihema cha mboni.


Mbendera ya chigono cha Rubeni ikhale kumwera monga mwa makamu ao; ndipo kalonga wa ana a Rubeni ndiye Elizuri mwana wa Sedeuri.


Mabanja a Ageresoni azimanga mahema ao pambuyo pa chihema kumadzulo.


Powawerenga amuna onse, kuyambira a mwezi umodzi ndi mphambu ndiwo zikwi zisanu ndi zitatu mphambu mazana asanu ndi limodzi, akusunga udikiro wa pamalo opatulika.


Ndipo kalonga wa nyumba ya makolo ao ya mabanja a Akohati ndiye Elizafani mwana wa Uziyele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa